Genesis 27:3 - Buku Lopatulika3 Tsopano tengatu zida zako ndi phodo lako ndi uta wako, numuke kuthengo kundisakira ine nyama: Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Tsopano tengatu zida zako ndi phodo lako ndi uta wako, numuke kuthengo kundisakira ine nyama: Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Tenga zida zako, uta ndi mivi yomwe, upite ku thengo ukandiphere nyama. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Tsono tenga zida zako, muvi wako ndi uta, pita kuthengo ukandiphere nyama. Onani mutuwo |