Genesis 27:4 - Buku Lopatulika4 nundikonzere ine chakudya chokolera chonga chomwe ndichikonda ine, nudze nacho kwa ine kuti ndidzadye; kuti moyo wanga ukadalitse iwe ndisanafe. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 nundikonzere ine chakudya chokolera chonga chomwe ndichikonda ine, nudze nacho kwa ine kuti ndidzadye; kuti moyo wanga ukadalitse iwe ndisanafe. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Undiphikire chakudya chokoma chija ndimakondachi, ubwere nacho kuno. Nditadya, ndidzakudalitsa ndisanafe.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Undikonzere chakudya chabwino monga muja ndimakonderamu ndipo ubwere nacho kwa ine kuti ndidye ndi kuti ndikudalitse ndisanamwalire.” Onani mutuwo |