Genesis 27:5 - Buku Lopatulika5 Ndipo anamva Rebeka pamene Isaki ananena ndi Esau mwana wake. Ndipo Esau ananka kuthengo kukasaka nyama ndi kubwera nayo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Ndipo anamva Rebeka pamene Isaki ananena ndi Esau mwana wake. Ndipo Esau ananka kuthengo kukasaka nyama ndi kubwera nayo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Rebeka ankangomvetsera pamene Isaki ankalankhula ndi mwana wake Esau. Tsono Esauyo atapita ku thengo kukasaka nyama yoti akapatse bambo wake, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Koma Rebeka amamvetsera pamene Isake amayankhula ndi mwana wake Esau. Esau atanyamuka kupita kuthengo kukaphera abambo ake nyama, Onani mutuwo |