Genesis 27:6 - Buku Lopatulika6 Ndipo Rebeka ananena kwa Yakobo mwana wake, nati, Taona ndinamva atate wako alimkunena ndi Esau mkulu wako kuti, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Ndipo Rebeka ananena kwa Yakobo mwana wake, nati, Taona ndinamva atate wako alimkunena ndi Esau mkulu wako kuti, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Rebeka adauza Yakobe kuti, “Ine ndamva bambo wako akuuza Esau kuti, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Rebeka anati kwa mwana wake Yakobo, “Taona ndamva abambo ako akuwuza mʼbale wako Esau kuti, Onani mutuwo |