Genesis 27:3 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Tsono tenga zida zako, muvi wako ndi uta, pita kuthengo ukandiphere nyama. Onani mutuwoBuku Lopatulika3 Tsopano tengatu zida zako ndi phodo lako ndi uta wako, numuke kuthengo kundisakira ine nyama: Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Tsopano tengatu zida zako ndi phodo lako ndi uta wako, numuke kuthengo kundisakira ine nyama: Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Tenga zida zako, uta ndi mivi yomwe, upite ku thengo ukandiphere nyama. Onani mutuwo |