Genesis 27:2 - Buku Lopatulika2 Ndipo anati, Taonatu, ndakalamba, sindidziwa tsiku la kufa kwanga: Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Ndipo anati, Taonatu, ndakalamba, sindidziwa tsiku la kufa kwanga: Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Tsono Isakiyo adati, “Ona, ine nkukalamba kuno, ndipo sindidziŵa tsiku loti ndidzafe. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Isake anati, “Tsopano ine ndakalamba, ndipo sindidziwa tsiku langa lakufa. Onani mutuwo |