Genesis 13:4 - Buku Lopatulika4 kumalo kwa guwa la nsembe analimanga iye kumeneko, poyamba paja; ndipo pamenepo Abramu anaitanira dzina la Yehova. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 kumalo kwa guwa la nsembe analimanga iye kumeneko, poyamba paja; ndipo pamenepo Abramu anaitanira dzina la Yehova. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Tsono adabwereranso ku malo aja kumene kale adaamangako guwa, ndipo adatama dzina la Chauta mopemba. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 ndiponso kumene Abramu anamangira Yehova guwa lansembe kwa nthawi yoyamba ndi kupemphera mʼdzina la Yehova. Onani mutuwo |