Genesis 10:1 - Buku Lopatulika1 Mibadwo ya ana a Nowa, Semu, Hamu ndi Yafeti, ndi iyi; kwa iwo ndipo kunabadwa ana aamuna, chitapita chigumula chija. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Mibadwo ya ana a Nowa, Semu, Hamu ndi Yafeti, ndi iyi; kwa iwo ndipo kunabadwa ana amuna, chitapita chigumula chija. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Nayi mibadwo ya ana a Nowa: Semu, Hamu ndi Yafeti. Atatu ameneŵa adabereka ana ao chitatha chigumula chija. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Nayi mbiri ya ana a Nowa, Semu, Hamu ndi Yafeti. Ana atatuwa anabereka ana awo chitatha chigumula. Onani mutuwo |