Genesis 10:2 - Buku Lopatulika2 Ana aamuna a Yafeti: Gomeri, ndi Magogi, ndi Madai, ndi Yavani, ndi Tubala, ndi Meseki ndi Tirasi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Ana amuna a Yafeti: Gomeri, ndi Magogi, ndi Madai, ndi Yavani, ndi Tubala, ndi Meseki ndi Tirasi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Ana a Yafeti anali Gomeri, Magogi, Madai, Yavani, Tubala, Meseki ndi Tirasi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Ana aamuna a Yafeti anali: Gomeri, Magogi, Madai, Yavani, Tubala, Mesaki ndi Tirasi. Onani mutuwo |
Ndipo ndidzaika chizindikiro pakati pao, ndipo ndidzatumiza onse amene apulumuka mwa iwo kwa amitundu, kwa Tarisisi, kwa Puti ndi kwa Aludi, okoka uta kwa Tubala ndi Yavani, kuzisumbu zakutali, amene sanamve mbiri yanga, ngakhale kuona ulemerero wanga; ndipo adzabukitsa ulemerero wanga pakati pa amitundu.