Genesis 10:3 - Buku Lopatulika3 Ndi ana aamuna a Gomeri: Asikenazi, ndi Rifati, ndi Togarima. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Ndi ana amuna a Gomeri: Asikenazi, ndi Rifati, ndi Togarima. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Ana a Gomeri anali Asikenazi, Rifati ndi Togarima. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Ana aamuna a Gomeri anali: Asikenazi, Rifati ndi Togarima. Onani mutuwo |