Genesis 10:3 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Ana aamuna a Gomeri anali: Asikenazi, Rifati ndi Togarima. Onani mutuwoBuku Lopatulika3 Ndi ana aamuna a Gomeri: Asikenazi, ndi Rifati, ndi Togarima. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Ndi ana amuna a Gomeri: Asikenazi, ndi Rifati, ndi Togarima. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Ana a Gomeri anali Asikenazi, Rifati ndi Togarima. Onani mutuwo |
“Kwezani mbendera ya nkhondo mʼdziko! Lizani lipenga pakati pa mitundu ya anthu! Konzekeretsani mitundu ya anthu kuti ikamuthire nkhondo; itanani maufumu awa: Ararati, Mini ndi Asikenazi kuti adzamuthire nkhondo. Ikani mtsogoleri wankhondo kuti amenyane naye; tumizani akavalo ochuluka ngati magulu a dzombe.