Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Genesis 10:1 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

1 Nayi mbiri ya ana a Nowa, Semu, Hamu ndi Yafeti. Ana atatuwa anabereka ana awo chitatha chigumula.

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

1 Mibadwo ya ana a Nowa, Semu, Hamu ndi Yafeti, ndi iyi; kwa iwo ndipo kunabadwa ana aamuna, chitapita chigumula chija.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

1 Mibadwo ya ana a Nowa, Semu, Hamu ndi Yafeti, ndi iyi; kwa iwo ndipo kunabadwa ana amuna, chitapita chigumula chija.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

1 Nayi mibadwo ya ana a Nowa: Semu, Hamu ndi Yafeti. Atatu ameneŵa adabereka ana ao chitatha chigumula chija.

Onani mutuwo Koperani




Genesis 10:1
12 Mawu Ofanana  

Ana aamuna a Yafeti anali: Gomeri, Magogi, Madai, Yavani, Tubala, Mesaki ndi Tirasi.


Mbiri ya momwe kumwamba ndi dziko lapansi zinalengedwera pa tsiku lija Yehova Mulungu ankazilenga ndi iyi: Yehova Mulungu atapanga dziko lapansi ndi kumwamba,


Ndondomeko ya mibado ya Adamu ndi iyi: Pamene Mulungu analenga munthu, anamulenga mʼchifaniziro cha Mulungu.


Pamene Nowa anali ndi zaka 500, anabereka Semu, Hamu ndi Yafeti.


Mbiri ya Nowa inali yotere: Nowa anali munthu wolungama ndi wopanda tchimo pakati pa anthu a mʼbado wake. Ndipo anayenda ndi Mulungu.


Ndipo Mulungu anadalitsa Nowa ndi ana ake aamuna nati kwa iwo, “Berekanani ndipo muchulukane ndi kudzaza dziko lapansi.


Ana aamuna a Nowa amenewa ndiwo anali makolo a anthu onse pa dziko lapansi.


Anamwalira ali ndi zaka 950.


Inu muberekane ndi kuchulukana kuti mudzaze dziko lonse lapansi ndi kuligonjetsa.”


Adamu, Seti, Enosi


Ana a Nowa, Semu, Hamu ndi Yafeti.


Buku lofotokoza za mʼbado wa Yesu Khristu mwana wa Davide, mwana wa Abrahamu:


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa