Genesis 9:29 - Buku Lopatulika29 Ndipo masiku onse a Nowa anali mazana asanu ndi anai kudza makumi asanu: ndipo anamwalira. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201429 Ndipo masiku onse a Nowa anali mazana asanu ndi anai kudza makumi asanu: ndipo anamwalira. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa29 Adamwalira ali wa zaka 950. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero29 Anamwalira ali ndi zaka 950. Onani mutuwo |