Genesis 9:28 - Buku Lopatulika28 Ndipo Nowa anakhala ndi moyo chigumula chitapita, zaka mazana atatu kudza makumi asanu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201428 Ndipo Nowa anakhala ndi moyo chigumula chitapita, zaka mazana atatu kudza makumi asanu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa28 Chitatha chigumulacho, Nowa adakhala ndi moyo zaka zina 350. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero28 Chitatha chigumula, Nowa anakhala ndi moyo zaka 350. Onani mutuwo |