Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Filemoni 1:4 - Buku Lopatulika

4 Ndiyamika Mulungu wanga nthawi zonse, ndi kukumbukira iwe m'mapemphero anga,

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

4 Ndiyamika Mulungu wanga nthawi zonse, ndi kukumbukira iwe m'mapemphero anga,

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

4 Ndimayamika Mulungu wanga nthaŵi zonse ndikamakukumbukira m'mapemphero anga.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

4 Ine ndimayamika Mulungu wanga nthawi zonse ndikakukumbukira iwe mʼmapemphero anga.

Onani mutuwo Koperani




Filemoni 1:4
8 Mawu Ofanana  

Poyamba, ndiyamika Mulungu wanga mwa Yesu Khristu chifukwa cha inu nonse, chifukwa kuti mbiri ya chikhulupiriro chanu idamveka padziko lonse lapansi.


sindileka kuyamika chifukwa cha inu, ndi kukumbukira inu m'mapemphero anga;


Ndiyamika Mulungu wanga pokumbukira inu ponse;


Tiyamika Mulungu Atate wa Ambuye wathu Yesu Khristu ndi kupempherera inu nthawi zonse,


Tiyamika Mulungu nthawi zonse chifukwa cha inu nonse, ndi kukumbukira inu m'mapemphero athu;


Tiziyamika Mulungu nthawi zonse chifukwa cha inu, abale, monga kuyenera; pakuti chikhulupiriro chanu chikula chikulire, ndipo chichulukira chikondano cha inu nonse, yense pa mnzake;


Ndiyamika Mulungu, amene ndimtumikira kuyambira makolo anga ndi chikumbumtima choyera, kuti ndikumbukira iwe kosalekeza m'mapemphero anga,


pakumva za chikondi chako ndi chikhulupiriro uli nacho chakulinga kwa Ambuye Yesu, ndi kwa oyera mtima onse;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa