Filemoni 1:3 - Buku Lopatulika3 Chisomo kwa inu ndi mtendere za kwa Mulungu Atate wathu ndi Ambuye Yesu Khristu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Chisomo kwa inu ndi mtendere za kwa Mulungu Atate wathu ndi Ambuye Yesu Khristu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Mulungu Atate athu ndi Ambuye Yesu Khristu akukomereni mtima ndi kukupatsani mtendere. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Chisomo ndi mtendere zochokera kwa Mulungu Atate athu ndi Ambuye Yesu Khristu zikhale ndi inu. Onani mutuwo |