Filemoni 1:2 - Buku Lopatulika2 ndi kwa Afiya mlongoyo, ndi Arkipo msilikali mnzathu, ndi kwa Mpingo uli m'nyumba yako: Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 ndi kwa Afiya mlongoyo, ndi Arkipo msilikali mnzathu, ndi kwa Mpingo uli m'nyumba yako: Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Kalata yomweyinso tikulembera Afiya, mlongo wathu, ndi Arkipo, msilikali mnzathu pa nkhondo ya Mulungu, ndiponso mpingo wonse umene umasonkhana kunyumba kwanu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Kwa Apiya mlongo wathu, Arkipo msilikali mnzathu, ndiponso mpingo umene umasonkhana mʼnyumba mwanu. Onani mutuwo |