Filemoni 1:4 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Ine ndimayamika Mulungu wanga nthawi zonse ndikakukumbukira iwe mʼmapemphero anga. Onani mutuwoBuku Lopatulika4 Ndiyamika Mulungu wanga nthawi zonse, ndi kukumbukira iwe m'mapemphero anga, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Ndiyamika Mulungu wanga nthawi zonse, ndi kukumbukira iwe m'mapemphero anga, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Ndimayamika Mulungu wanga nthaŵi zonse ndikamakukumbukira m'mapemphero anga. Onani mutuwo |