Filemoni 1:5 - Buku Lopatulika5 pakumva za chikondi chako ndi chikhulupiriro uli nacho chakulinga kwa Ambuye Yesu, ndi kwa oyera mtima onse; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 pakumva za chikondi chako ndi chikhulupiriro uli nacho chakulinga kwa Ambuye Yesu, ndi kwa oyera mtima onse; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Pakuti ndikumva kuti umakonda ndi kukhulupirira Ambuye Yesu, ndi oyera onse a Mulungu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Pakuti ndamva za chikondi chako, za chikhulupiriro chako mwa Ambuye Yesu ndiponso za chikondi chako pa oyera mtima onse. Onani mutuwo |