Filemoni 1:24 - Buku Lopatulika24 ateronso, Marko, Aristariko, Dema, Luka, antchito anzanga. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201424 ateronso, Marko, Aristariko, Dema, Luka, antchito anzanga. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa24 Akutinso moni anzanga antchito, Marko, Aristariko, Dema, ndi Luka. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero24 Atumiki anzanga awa, Marko, Aristariko, Dema ndi Luka, akuperekanso moni. Onani mutuwo |