Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Filemoni 1:25 - Buku Lopatulika

25 Chisomo cha Ambuye wathu Yesu Khristu chikhale pamodzi ndi mzimu wanu. Amen.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

25 Chisomo cha Ambuye wathu Yesu Khristu chikhale pamodzi ndi mzimu wanu. Amen.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

25 Ambuye Yesu Khristu akukomereni mtima nonse.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

25 Chisomo cha Ambuye Yesu Khristu chikhale ndi mzimu wako.

Onani mutuwo Koperani




Filemoni 1:25
4 Mawu Ofanana  

Ndipo Mulungu wa mtendere adzaphwanya Satana pansi pa mapazi anu tsopano lino. Chisomo cha Ambuye wathu Yesu Khristu chikhale ndi inu nonse.


Gayo, mwini nyumba wolandira ine, ndi Mpingo wonse wa Ambuye, akupereka moni. Erasto, ndiye woyang'anira mzinda, akupereka moni, ndiponso Kwarto mbaleyo.


Chisomo cha Ambuye wathu Yesu Khristu chikhale ndi mzimu wanu, abale. Amen.


Ambuye akhale ndi mzimu wako. Chisomo chikhale nanu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa