Filemoni 1:23 - Buku Lopatulika23 Epafra wandende mnzanga mwa Khristu Yesu akukupatsa moni; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201423 Epafra wandende mnzanga mwa Khristu Yesu akukupatsa moni; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa23 Akukupatsa moni Epafra, amene ali m'ndende pamodzi nane chifukwa cha Khristu Yesu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero23 Epafra, wamʼndende mnzanga chifukwa cha Khristu Yesu akupereka moni. Onani mutuwo |