Filemoni 1:21 - Buku Lopatulika21 Pokhulupirira kumvera kwako ndikulembera iwe, podziwa kuti udzachitanso koposa chimene ndinena. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201421 Pokhulupirira kumvera kwako ndikulembera iwe, podziwa kuti udzachitanso koposa chimene ndinena. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa21 Ndikukulembera zimenezi, popeza kuti ndikukhulupirira kuti udzachitadi zimene ndakupempha. Ndikudziŵa kuti udzachita kopitiriranso zimene ndapemphazi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero21 Ine ndili ndi chitsimikizo cha kumvera kwako pamene ndikukulembera kalatayi. Ndikulemba ndikudziwa kuti udzachita ngakhale kuposa zimene ndakupemphazi. Onani mutuwo |