Filemoni 1:18 - Buku Lopatulika18 Koma ngati anakulakwira kanthu, kapena wokongola kanthu, kanthu, kapena wakongola kanthu, undiwerengere ine kameneko; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 Koma ngati anakulakwira kanthu, kapena wokongola kanthu, kanthu, kapena wakongola kanthu, undiwerengere ine kameneko; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 Ngati adakulakwirapo, kapena ali ndi ngongole kwa iwe, ngongoleyo ikhale yanga. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 Ngati anakulakwira kapena kukongola kanthu kalikonse, ndidzalipira ineyo. Onani mutuwo |