Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Filemoni 1:18 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

18 Ngati anakulakwira kapena kukongola kanthu kalikonse, ndidzalipira ineyo.

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

18 Koma ngati anakulakwira kanthu, kapena wokongola kanthu, kanthu, kapena wakongola kanthu, undiwerengere ine kameneko;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

18 Koma ngati anakulakwira kanthu, kapena wokongola kanthu, kanthu, kapena wakongola kanthu, undiwerengere ine kameneko;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

18 Ngati adakulakwirapo, kapena ali ndi ngongole kwa iwe, ngongoleyo ikhale yanga.

Onani mutuwo Koperani




Filemoni 1:18
4 Mawu Ofanana  

Ine ndidzipereka kuti ndikhale chikole cha moyo wa mnyamatayu. Ine ndidzamuteteza. Ngati sindibwera naye ndi kumupereka kwa inu, ndidzakhala wolakwa pamaso panu moyo wanga wonse.


Tsono ngati umati ndine mnzako, umulandire iyeyu monga momwe ukanandilandirira ineyo.


Ine, Paulo ndikulemba zimenezi ndi dzanja langa. Ine ndidzalipira. Nʼkosafunika kukukumbutsa kuti iweyo ngongole yako kwa ine ndi moyo wakowo.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa