Filemoni 1:14 - Buku Lopatulika14 koma wopanda kudziwa mtima wako sindinafune kuchita kanthu; kuti ubwino wako usakhale monga mokakamiza, komatu mwaufulu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201414 koma wopanda kudziwa mtima wako sindinafuna kuchita kanthu; kuti ubwino wako usakhale monga mokakamiza, komatu mwaufulu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa14 Koma sindikufuna kuchita kanthu osakufunsa, kuwopa kuti ungandichitire chinthu chabwinochi mokakamizidwa, osati mwaufulu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero14 Koma sindikufuna kuchita kanthu osakufunsa, nʼcholinga chakuti chilichonse chabwino ungandichitire chikhale mwakufuna kwako osati mokakamiza. Onani mutuwo |