Filemoni 1:13 - Buku Lopatulika13 Ameneyo ndikadafuna ine kumsunga akhale nane, kuti m'malo mwako akadanditumikira ine m'ndende za Uthenga Wabwino: Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201413 Ameneyo ndikadafuna ine kumsunga akhale nane, kuti m'malo mwako akadanditumikira ine m'ndende za Uthenga Wabwino: Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa13 Ndikadakonda kuti akhalebe ndi ine kuno, kuti azinditumikira m'malo mwako, pokhala ndili m'ndende chifukwa cha Uthenga Wabwino. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero13 Ndikanakonda ndikanakhala naye kuno kuti iyeyo azinditumikira mʼmalo mwako pamene ndili mu unyolo chifukwa cha Uthenga Wabwino. Onani mutuwo |