Filemoni 1:12 - Buku Lopatulika12 amene ndi yemweyo ndakubwezera iwe, ndiye mtima weniweni wa ine. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 amene ndi yemweyo ndakubwezera iwe, ndiye mtima weniweni wa ine. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Ndikumtumizanso kwa iwe tsopano, ndipo pakutero ndikuchita ngati kukutumizira mtima wanga womwe. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Ine ndikumutumizanso kwa iwe tsopano, koma potero ndikukhala ngati ndikutumiza mtima wanga weniweni. Onani mutuwo |