Filemoni 1:11 - Buku Lopatulika11 amene kale sanakupindulire, koma tsopano watipindulira bwino iwe ndi ine; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 amene kale sanakupindulira, koma tsopano watipindulira bwino iwe ndi ine; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 Kale unalibe naye ntchito, koma tsopano angathe kutithandiza kwambiri tonsefe, iweyo ndi ine ndemwe. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 Anali wopanda phindu kwa iwe, koma tsopano wasanduka wa phindu kwa iwe ndi kwa inenso. Onani mutuwo |