Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Filemoni 1:11 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

11 Anali wopanda phindu kwa iwe, koma tsopano wasanduka wa phindu kwa iwe ndi kwa inenso.

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

11 amene kale sanakupindulire, koma tsopano watipindulira bwino iwe ndi ine;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

11 amene kale sanakupindulira, koma tsopano watipindulira bwino iwe ndi ine;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

11 Kale unalibe naye ntchito, koma tsopano angathe kutithandiza kwambiri tonsefe, iweyo ndi ine ndemwe.

Onani mutuwo Koperani




Filemoni 1:11
10 Mawu Ofanana  

Ndipo muponyeni wantchito wopanda phinduyu kunja, ku mdima kumene kudzakhala kulira ndi kukukuta mano.’ ”


Pakuti mwana wangayu anali wakufa, ndipo ali ndi moyonso; iye anatayika ndipo wapezeka.’ Chomwecho anayamba kukondwerera.


Koma tinayenera kukondwera ndi kusangalala, chifukwa mʼbale wako uyu anali wakufa ndipo ali ndi moyonso; iye anali wotayika ndipo wapezeka.”


Chimodzimodzi inunso, mukachita zonse zimene munawuzidwa, muzinena kuti, ‘Ndife antchito osayenera; tangogwira ntchito yathu basi.’ ”


Onse apatukira kumbali, onse pamodzi asanduka opandapake. Palibe ndi mmodzi yemwe amene amachita zabwino, palibe ngakhale mmodzi.”


Ndatsala ndi Luka yekha basi. Mutenge Marko ndipo ubwere naye kuno, chifukwa amandithandiza mu utumiki wanga.


ndikukupempha chifukwa cha mwana wanga Onesimo, amene ndamubala ndili mu unyolo.


Ine ndikumutumizanso kwa iwe tsopano, koma potero ndikukhala ngati ndikutumiza mtima wanga weniweni.


Kale simunali anthu ake, koma tsopano ndinu anthu a Mulungu. Kale simunalandire chifundo, koma tsopano mwalandira chifundo.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa