Filemoni 1:15 - Buku Lopatulika15 Pakuti kapena anasiyanitsidwa ndi iwe kanthawi chifukwa cha ichi, ndi kuti udzakhala naye nthawi zonse; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201415 Pakuti kapena anasiyanitsidwa ndi iwe kanthawi chifukwa cha ichi, ndi kuti udzakhala naye nthawi zonse; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa15 Kapena Onesimo adangokusiya kanthaŵi pang'ono, kuti udzakhale naye nthaŵi zonse, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero15 Mwina chifukwa chimene unasiyana naye kwa kanthawi ndi chakuti ukhale nayenso nthawi zonse. Onani mutuwo |