Filemoni 1:15 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero15 Mwina chifukwa chimene unasiyana naye kwa kanthawi ndi chakuti ukhale nayenso nthawi zonse. Onani mutuwoBuku Lopatulika15 Pakuti kapena anasiyanitsidwa ndi iwe kanthawi chifukwa cha ichi, ndi kuti udzakhala naye nthawi zonse; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201415 Pakuti kapena anasiyanitsidwa ndi iwe kanthawi chifukwa cha ichi, ndi kuti udzakhala naye nthawi zonse; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa15 Kapena Onesimo adangokusiya kanthaŵi pang'ono, kuti udzakhale naye nthaŵi zonse, Onani mutuwo |