Eksodo 6:29 - Buku Lopatulika29 Yehova ananena ndi Mose, ndi kuti, Ine ndine Yehova; lankhula ndi Farao mfumu ya Aejipito zonsezi Ine ndizinena nawe. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201429 Yehova ananena ndi Mose, ndi kuti, Ine ndine Yehova; lankhula ndi Farao mfumu ya Aejipito zonsezi Ine ndizinena nawe. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa29 adati “Ine ndine Chauta. Ukamuuze Farao, mfumu ya ku Ejipito, zonse zimene ndikuuze.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero29 anati, “Ine ndine Yehova. Umuwuze Farao mfumu ya Igupto zonse zimene Ine ndikuwuze iwe.” Onani mutuwo |