Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Eksodo 6:28 - Buku Lopatulika

28 Ndipo kunali, tsiku limene Yehova ananena ndi Mose m'dziko la Ejipito,

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

28 Ndipo kunali, tsiku limene Yehova ananena ndi Mose m'dziko la Ejipito,

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

28 Pamene Chauta adalankhula ndi Mose ku dziko la Ejipito,

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

28 Tsopano pamene Yehova anayankhula kwa Mose mu Igupto,

Onani mutuwo Koperani




Eksodo 6:28
2 Mawu Ofanana  

Awa ndi omwewo ananena ndi Farao, mfumu ya Aejipito, awatulutse ana a Israele mu Ejipito; Mose ndi Aroni amenewa.


Yehova ananena ndi Mose, ndi kuti, Ine ndine Yehova; lankhula ndi Farao mfumu ya Aejipito zonsezi Ine ndizinena nawe.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa