Eksodo 6:30 - Buku Lopatulika30 Koma Mose anati pamaso pa Yehova, Onani, ine ndili wa milomo yosadula ndipo Farao adzandimvera bwanji? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201430 Koma Mose anati pamaso pa Yehova, Onani, ine ndili wa milomo yosadula ndipo Farao adzandimvera bwanji? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa30 Koma Mose adauza Chauta kuti, “Inu mukudziŵa kuti paja ndine wosakhoza kulankhula, nanga Faraoyo adzandimvera bwanji?” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero30 Koma Mose anati kwa Yehova, “Farao akandimvera bwanji, pakuti ine sinditha kuyankhula bwino?” Onani mutuwo |