Eksodo 6:18 - Buku Lopatulika18 Ndi ana aamuna a Kohati ndiwo: Amuramu ndi Izihara, ndi Hebroni, ndi Uziyele; ndipo zaka za moyo wa Kohati ndizo zana limodzi ndi makumi atatu ndi kudza zitatu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 Ndi ana amuna a Kohati ndiwo: Amuramu ndi Izihara, ndi Hebroni, ndi Uziyele; ndipo zaka za moyo wa Kohati ndizo zana limodzi ndi makumi atatu ndi kudza zitatu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 Ana a Kohati naŵa: Amuramu, Izihara, Hebroni ndi Uziyele. Kohati adakhala zaka 133 ali moyo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 Ana a Kohati anali Amramu, Izihari, Hebroni ndi Uzieli. Kohati anakhala ndi moyo zaka 133. Onani mutuwo |