Eksodo 6:19 - Buku Lopatulika19 Ndipo ana aamuna a Merari ndiwo: Mali ndi Musi. Amenewo ndiwo mabanja a Levi mwa kubadwa kwao. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201419 Ndipo ana amuna a Merari ndiwo: Mali ndi Musi. Amenewo ndiwo mabanja a Levi mwa kubadwa kwao. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa19 Ana a Merari naŵa: Mali ndi Musi. Ameneŵa ndiwo mabanja a Levi pamodzi ndi zidzukulu zao. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero19 Ana a Merari anali Mali ndi Musi. Awa anali mafuko a Levi monga mwa mibado yawo. Onani mutuwo |