Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Eksodo 6:17 - Buku Lopatulika

17 Ana aamuna a Geresoni ndiwo: Libini ndi Simei, mwa mabanja ao.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

17 Ana amuna a Geresoni ndiwo: Libini ndi Simei, mwa mabanja ao.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

17 Ana a Geresoni naŵa: Libini ndi Simeyi pamodzi ndi mabanja ao.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

17 Ana a Geresoni, mwa mafuko awo, anali Libini ndi Simei.

Onani mutuwo Koperani




Eksodo 6:17
6 Mawu Ofanana  

Ndi ana aamuna a Levi: Geresoni, Kohati, ndi Merari.


A Ageresoni: Ladani ndi Simei.


Ndipo maina a ana a Geresomo ndi awa: Libini, ndi Simei.


Ana a Merari: Mali, Libini mwana wake, Simei mwana wake, Uza mwana wake,


Ndi ana a Geresoni maina ao ndi awa, monga mwa mabanja ao: Libini, ndi Simei.


Ndipo ana a Geresoni analandira molota maere motapa pa mabanja a fuko la Isakara, ndi pa fuko la Asere, ndi pa fuko la Nafutali, ndi pa hafu la fuko la Manase mu Basani, mizinda khumi ndi itatu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa