Eksodo 5:23 - Buku Lopatulika23 Popeza kuyambira kuja ndinafika kwa Farao kulankhula m'dzina lanu, anawachitira choipa anthuwa; ndipo simunalanditse anthu anu konse. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201423 Popeza kuyambira kuja ndinafika kwa Farao kulankhula m'dzina lanu, anawachitira choipa anthuwa; ndipo simunalanditsa anthu anu konse. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa23 Chipitire changa chija kwa Farao kukamuuza mau anu aja, wakhala akuzunzabe anthu anu. Ndipo Inu simudachitepo kanthu konse kuti muŵaombole anthu anu.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero23 Chipitireni changa kwa Farao kukamuyankhula mʼdzina lanu, iye wakhala akuzunza anthuwa, ndipo inu simunawapulumutse konse anthu anu.” Onani mutuwo |