Eksodo 40:8 - Buku Lopatulika8 Ndipo ukamange mpandawo pozungulira, ndi kupachika nsalu yotsekera pa chipata cha pabwalo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Ndipo ukamange mpandawo pozungulira, ndi kupachika nsalu yotsekera pa chipata cha pabwalo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Upange bwalo kuzungulira chihemacho, ndi kukoloŵeka nsalu zochingira pa chipata chake cha bwalolo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Upange bwalo lozungulira chihemacho ndipo uyike katani ya pa chipata cha bwalolo. Onani mutuwo |