Eksodo 40:7 - Buku Lopatulika7 Ukaikenso mkhate pakati pa chihema chokomanako, ndi guwa la nsembe, ndi kuthiramo madzi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Ukaikenso mkhate pakati pa chihema chokomanako, ndi guwa la nsembe, ndi kuthiramo madzi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Beseni uliike pakati pa chihema chamsonkhano ndi guwa, ndipo uthiremo madzi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Uyike beseni pakati pa tenti ya msonkhano ndi guwa lansembe ndipo uyikemo madzi. Onani mutuwo |