Eksodo 40:6 - Buku Lopatulika6 Ndipo ukaike guwa la nsembe yopsereza kunja kwa khomo la Kachisi wa chihema chokomanako. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Ndipo ukaike guwa la nsembe yopsereza kunja kwa khomo la Kachisi wa chihema chokomanako. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Uike guwa lootcherapo nsembe patsogolo pa chihema chamsonkhanocho. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 “Uyike guwa lansembe yopsereza patsogolo pa chipata cha chihema, tenti ya msonkhano. Onani mutuwo |