Eksodo 40:5 - Buku Lopatulika5 Ndipo ukaike guwa la nsembe lofukizapo lagolide chakuno cha likasa la mboni, numange pa chihema nsalu yotsekera pakhomo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Ndipo ukaike guwa la nsembe lofukizapo lagolide chakuno cha likasa la mboni, numange pa Kachisi nsalu yotsekera pakhomo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Tsono uike guwa lagolide lofukizirapo lubani patsogolo pa bokosi laumboni. Pa chipata cha Nyumba ya Mulungu utsekepo ndi nsalu zochinga. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Uyike guwa lofukiza la golide patsogolo pa bokosi la umboni ndipo uyike katani ya pa chipata cha chihema. Onani mutuwo |