Eksodo 40:4 - Buku Lopatulika4 Ulongenso gomelo, nukonzerepo zokonzera zake; ulongenso choikaponyalicho, ndi kuyatsa nyali zake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Ulongenso gomelo, nukonzerepo zokonzera zake; ulongenso choikapo nyalicho, ndi kuyatsa nyali zake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Ukhazikemonso tebulo, pamwamba pake uikepo zipangizo zake, ndipo uikemo choikaponyale ndi nyale zake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Ulowetsemo tebulo ndi kuyika zimene zimakhala pamenepo. Kenaka ulowetse choyikapo nyale ndipo uyikepo nyale zake. Onani mutuwo |