Eksodo 40:3 - Buku Lopatulika3 Ndipo ukaikemo likasa la mboni, nutchinge likasalo ndi nsalu yotchingayo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Ndipo ukaikemo likasa la mboni, nuchinge likasalo ndi nsalu yotchingayo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Bokosi m'mene muli miyala yaumboni uliike m'menemo, ndipo bokosilo uliphimbe ndi nsalu kuti ulichinge. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Uyikemo bokosi la umboni ndipo uphimbe bokosilo ndi katani. Onani mutuwo |