Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Eksodo 40:4 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

4 Ulowetsemo tebulo ndi kuyika zimene zimakhala pamenepo. Kenaka ulowetse choyikapo nyale ndipo uyikepo nyale zake.

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

4 Ulongenso gomelo, nukonzerepo zokonzera zake; ulongenso choikaponyalicho, ndi kuyatsa nyali zake.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

4 Ulongenso gomelo, nukonzerepo zokonzera zake; ulongenso choikapo nyalicho, ndi kuyatsa nyali zake.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

4 Ukhazikemonso tebulo, pamwamba pake uikepo zipangizo zake, ndipo uikemo choikaponyale ndi nyale zake.

Onani mutuwo Koperani




Eksodo 40:4
7 Mawu Ofanana  

“Lamula Aisraeli kuti akupatse mafuta anyale a olivi wabwino kwambiri kuti nyalezo ziziyaka nthawi zonse.


Sabata ndi sabata nthawi zonse Aaroni aziyika makeke amenewa pamaso pa Yehova mʼmalo mwa Aisraeli onse kuti akhale pangano lamuyaya.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa