Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Eksodo 40:5 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

5 Uyike guwa lofukiza la golide patsogolo pa bokosi la umboni ndipo uyike katani ya pa chipata cha chihema.

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

5 Ndipo ukaike guwa la nsembe lofukizapo lagolide chakuno cha likasa la mboni, numange pa chihema nsalu yotsekera pakhomo.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

5 Ndipo ukaike guwa la nsembe lofukizapo lagolide chakuno cha likasa la mboni, numange pa Kachisi nsalu yotsekera pakhomo.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

5 Tsono uike guwa lagolide lofukizirapo lubani patsogolo pa bokosi laumboni. Pa chipata cha Nyumba ya Mulungu utsekepo ndi nsalu zochinga.

Onani mutuwo Koperani




Eksodo 40:5
12 Mawu Ofanana  

Uyike guwalo patsogolo pa nsalu yotchinga Bokosi la Chipangano. Apa ndi pamene ndizidzakumana nawe.


“Uyike guwa lansembe yopsereza patsogolo pa chipata cha chihema, tenti ya msonkhano.


Pamene anthu akusamuka pa msasa, Aaroni ndi ana ake aamuna azilowa mu tenti ndi kuchotsa chinsalu chotchingira ndi kuphimba nacho bokosi la umboni.


Yesu anayankha kuti, “Ine ndine njira, choonadi ndi moyo. Palibe munthu angafike kwa Atate popanda kudzera mwa Ine.


Pakuti Khristu sanalowe mʼmalo opatulika omangidwa ndi anthu amene anali chifaniziro cha malo enieniwo. Iye analowa kumwamba kwenikweniko kuti azionekera pamaso pa Mulungu chifukwa cha ife.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa