Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Eksodo 40:8 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

8 Upange bwalo lozungulira chihemacho ndipo uyike katani ya pa chipata cha bwalolo.

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

8 Ndipo ukamange mpandawo pozungulira, ndi kupachika nsalu yotsekera pa chipata cha pabwalo.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

8 Ndipo ukamange mpandawo pozungulira, ndi kupachika nsalu yotsekera pa chipata cha pabwalo.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

8 Upange bwalo kuzungulira chihemacho, ndi kukoloŵeka nsalu zochingira pa chipata chake cha bwalolo.

Onani mutuwo Koperani




Eksodo 40:8
8 Mawu Ofanana  

Kenaka Mose anamanga bwalo kuzungulira chihema ndi guwa lansembe ndipo anayika katani ya pa chipata cha bwalo. Kotero Mose anamaliza ntchito.


Uyike beseni pakati pa tenti ya msonkhano ndi guwa lansembe ndipo uyikemo madzi.


“Utenge mafuta wodzozera ndipo udzoze chihema ndi chilichonse chili mʼmenemo ndipo zidzakhala zoyeretsedwa.


Ndipo Ine ndikuwuza iwe kuti ndiwe Petro ndipo pa thanthwe ili Ine ndidzamangapo mpingo wanga ndipo makomo a ku gehena sadzawugonjetsa.


Ndipo Mulungu mu mpingo anayika poyamba atumwi, kachiwiri aneneri, kachitatu aphunzitsi, kenaka ochita zozizwitsa, ena a mphatso zamachiritso, ena a mphatso yothandiza anzawo, ena a mphatso yotsogolera ndiponso ena a mphatso ya malilime.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa