Eksodo 4:4 - Buku Lopatulika4 Koma Yehova anati kwa Mose, Tambasula dzanja lako, nuigwire kumchira; ndipo anatambasula dzanja lake, naigwira, nikhalanso ndodo m'dzanja lake; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Koma Yehova anati kwa Mose, Tambasula dzanja lako, nuigwire kumchira; ndipo anatambasula dzanja lake, naigwira, nikhalanso ndodo m'dzanja lake; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Apo Chauta adauza Mose uja kuti, “Igwire mchira.” Mose adaigwira, pompo idasandukanso ndodo m'manja mwakemo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Kenaka Yehova anati kwa iye, “Igwire mtchira.” Ndipo Mose anayigwira mchira njokayo ndipo inasandukanso ndodo mʼdzanja lake. Onani mutuwo |