Eksodo 4:4 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Kenaka Yehova anati kwa iye, “Igwire mtchira.” Ndipo Mose anayigwira mchira njokayo ndipo inasandukanso ndodo mʼdzanja lake. Onani mutuwoBuku Lopatulika4 Koma Yehova anati kwa Mose, Tambasula dzanja lako, nuigwire kumchira; ndipo anatambasula dzanja lake, naigwira, nikhalanso ndodo m'dzanja lake; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Koma Yehova anati kwa Mose, Tambasula dzanja lako, nuigwire kumchira; ndipo anatambasula dzanja lake, naigwira, nikhalanso ndodo m'dzanja lake; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Apo Chauta adauza Mose uja kuti, “Igwire mchira.” Mose adaigwira, pompo idasandukanso ndodo m'manja mwakemo. Onani mutuwo |